1 Atesalonika 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti inu nonse ndinu ana a kuwala+ ndiponso ana a usana.+ Si ife a usiku kapena a mdima ayi.+