2 Atesalonika 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Choncho abale, khalani olimba+ ndipo gwirani mwamphamvu miyambo+ imene munaphunzitsidwa, kaya mwa uthenga wapakamwa kapena mwa kalata yochokera kwa ife. 2 Atesalonika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:15 Nsanja ya Olonda,12/15/2013, ptsa. 8-9
15 Choncho abale, khalani olimba+ ndipo gwirani mwamphamvu miyambo+ imene munaphunzitsidwa, kaya mwa uthenga wapakamwa kapena mwa kalata yochokera kwa ife.