1 Timoteyo 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tikudziwa kuti Chilamulo n’chabwino+ ngati munthu akuchigwiritsa ntchito moyenera.+