-
1 Timoteyo 6:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Komanso, akapolo amene ambuye awo ndi okhulupirira,+ asamawapeputse+ chifukwa chakuti ndi abale.+ M’malomwake, akhale akapolo odzipereka kwambiri, pakuti amene akupindula ndi utumiki wawo wabwinowo ndi okhulupirira ndiponso okondedwa.
Pitiriza kuwaphunzitsa ndi kuwadandaulira kuti azichita zimenezi.+
-