Akolose 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Inu anthu amene muli ambuye, pitirizani kuchitira akapolo+ anu zinthu zachilungamo ndi zoyenera, podziwa kuti inunso muli ndi Ambuye kumwamba.+
4 Inu anthu amene muli ambuye, pitirizani kuchitira akapolo+ anu zinthu zachilungamo ndi zoyenera, podziwa kuti inunso muli ndi Ambuye kumwamba.+