2 Timoteyo 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pamene ndinali kudziteteza koyamba pa mlandu wanga, palibe amene anakhala kumbali yanga. Onse anandisiya ndekha.+ Ngakhale zinali choncho, usakhale mlandu kwa iwo.+ 2 Timoteyo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:16 Nsanja ya Olonda,4/15/2015, ptsa. 24-25
16 Pamene ndinali kudziteteza koyamba pa mlandu wanga, palibe amene anakhala kumbali yanga. Onse anandisiya ndekha.+ Ngakhale zinali choncho, usakhale mlandu kwa iwo.+