Aroma 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wodala ndi munthu amene Yehova sadzawerengera tchimo lake.”+ 1 Akorinto 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 sichichita zosayenera,+ sichisamala zofuna zake zokha,+ sichikwiya.+ Sichisunga zifukwa.+