Salimo 32:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Wodala ndi munthu amene Yehova sanamusungire cholakwa chake,+Amene alibe mtima wachinyengo.+ 2 Akorinto 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Utumiki wake ndi woti tilengeze kuti Mulungu anali kugwirizanitsa dziko+ ndi iyeyo+ kudzera mwa Khristu,+ moti sanawawerengere anthuwo machimo awo,+ ndipo watipatsa ifeyo ntchito yolengeza uthenga+ umenewu wokhazikitsanso mtendere.+
19 Utumiki wake ndi woti tilengeze kuti Mulungu anali kugwirizanitsa dziko+ ndi iyeyo+ kudzera mwa Khristu,+ moti sanawawerengere anthuwo machimo awo,+ ndipo watipatsa ifeyo ntchito yolengeza uthenga+ umenewu wokhazikitsanso mtendere.+