Tito 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tizichita zimenezi pamene tikuyembekeza kukwaniritsidwa kwa chiyembekezo+ chosangalatsa ndi kuonetsedwa kwaulemerero+ kwa Mulungu wamkuluyo ndiponso kwa Mpulumutsi wathu, Khristu Yesu. Tito Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:13 Nsanja ya Olonda,11/15/2011, tsa. 20 Kukambitsirana, tsa. 408
13 Tizichita zimenezi pamene tikuyembekeza kukwaniritsidwa kwa chiyembekezo+ chosangalatsa ndi kuonetsedwa kwaulemerero+ kwa Mulungu wamkuluyo ndiponso kwa Mpulumutsi wathu, Khristu Yesu.