Aheberi 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti dziko lapansi lokhalamo anthu limene likubweralo,+ limene ife tikunena, sanaliike pansi pa ulamuliro wa angelo. Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:5 Nsanja ya Olonda,8/15/2009, tsa. 114/1/1994, ptsa. 6-7
5 Pakuti dziko lapansi lokhalamo anthu limene likubweralo,+ limene ife tikunena, sanaliike pansi pa ulamuliro wa angelo.