Yesaya 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Sizidzavulazana+ kapena kuwonongana m’phiri langa lonse loyera,+ chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa Yehova ngati mmene madzi amadzazira nyanja.+ Machitidwe 17:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.” 2 Petulo 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma pali kumwamba kwatsopano+ ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ife tikuyembekezera mogwirizana ndi lonjezo lake, ndipo mmenemo mudzakhala chilungamo.+
9 Sizidzavulazana+ kapena kuwonongana m’phiri langa lonse loyera,+ chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa Yehova ngati mmene madzi amadzazira nyanja.+
31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ m’chilungamo dziko lapansi kumene kuli anthu, kudzera mwa munthu amene iye wamuika. Ndipo wapereka chitsimikizo kwa anthu onse mwa kumuukitsa+ kwa akufa.”
13 Koma pali kumwamba kwatsopano+ ndi dziko lapansi latsopano+ zimene ife tikuyembekezera mogwirizana ndi lonjezo lake, ndipo mmenemo mudzakhala chilungamo.+