Aheberi 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Komanso, kodi Mulungu ananyansidwa ndi ndani kwa zaka 40?+ Kodi sananyansidwe ndi anthu amene anachimwa aja, amene anafera m’chipululu?+
17 Komanso, kodi Mulungu ananyansidwa ndi ndani kwa zaka 40?+ Kodi sananyansidwe ndi anthu amene anachimwa aja, amene anafera m’chipululu?+