Aheberi 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero, popeza lonjezo lolowa mu mpumulo wake lidakalipo,+ samalani kuopera kuti pa nthawi ina, wina wa inu angalephere kukwaniritsa zofunika kuti akalowe mu mpumulowo.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:1 Nsanja ya Olonda,7/15/2011, ptsa. 26-277/15/1998, tsa. 17
4 Chotero, popeza lonjezo lolowa mu mpumulo wake lidakalipo,+ samalani kuopera kuti pa nthawi ina, wina wa inu angalephere kukwaniritsa zofunika kuti akalowe mu mpumulowo.+