Aheberi 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiye kunena za zinthu zimene tikukambiranazi, mfundo yaikulu ndi iyi: Tili ndi mkulu wa ansembe+ ngati ameneyu, ndipo iye wakhala pansi kumwamba, kudzanja lamanja la mpando wachifumu wa Wolemekezeka.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:1 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 161 Sukulu ya Utumiki, ptsa. 29-31
8 Ndiye kunena za zinthu zimene tikukambiranazi, mfundo yaikulu ndi iyi: Tili ndi mkulu wa ansembe+ ngati ameneyu, ndipo iye wakhala pansi kumwamba, kudzanja lamanja la mpando wachifumu wa Wolemekezeka.+