Aheberi 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Pangano limene ndidzapangana ndi nyumba ya Isiraeli pambuyo pa pangano loyamba lija ndi ili: Ndidzaika malamulo anga m’maganizo mwawo ndi kuwalemba m’mitima yawo.+ Ine ndidzakhala Mulungu wawo+ ndipo iwo adzakhala anthu anga,’+ watero Yehova. Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:10 Chisungiko cha Padziko Lonse, ptsa. 113-114
10 “‘Pangano limene ndidzapangana ndi nyumba ya Isiraeli pambuyo pa pangano loyamba lija ndi ili: Ndidzaika malamulo anga m’maganizo mwawo ndi kuwalemba m’mitima yawo.+ Ine ndidzakhala Mulungu wawo+ ndipo iwo adzakhala anthu anga,’+ watero Yehova.