11 Komabe, pamene Khristu anabwera monga mkulu wa ansembe,+ wa zinthu zabwino zimene zakwaniritsidwa, anatero kudzera m’chihema chachikulu ndi changwiro kwambiri chimene sichinapangidwe ndi manja a anthu, kutanthauza kuti, sichili mbali ya chilengedwe chapansi pano.+