1 Yohane 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ife ndife ochokera kwa Mulungu.+ Amene amadziwa Mulungu amatimvera,+ ndipo amene sachokera kwa Mulungu satimvera.+ Mmenemu ndi mmene timadziwira mawu ouziridwa oona kapena abodza.+ 1 Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:6 Nsanja ya Olonda,2/1/1987, tsa. 13
6 Ife ndife ochokera kwa Mulungu.+ Amene amadziwa Mulungu amatimvera,+ ndipo amene sachokera kwa Mulungu satimvera.+ Mmenemu ndi mmene timadziwira mawu ouziridwa oona kapena abodza.+