Chivumbulutso 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ine Yohane, m’bale wanu ndi wogawana nanu masautso+ a Yesu,+ mu ufumu+ ndi m’kupirira,+ ndinali pachilumba cha Patimo chifukwa cholankhula za Mulungu ndi kuchitira umboni za Yesu.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:9 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 20-21 Nsanja ya Olonda,12/1/1999, ptsa. 14-15
9 Ine Yohane, m’bale wanu ndi wogawana nanu masautso+ a Yesu,+ mu ufumu+ ndi m’kupirira,+ ndinali pachilumba cha Patimo chifukwa cholankhula za Mulungu ndi kuchitira umboni za Yesu.+