Chivumbulutso 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso, mutu ndi tsitsi lake zinali zoyera+ ngati ubweya wa nkhosa woyera, zoyera kwambiri kuti mbee! Ndipo maso ake anali ngati lawi la moto.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:14 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 25
14 Komanso, mutu ndi tsitsi lake zinali zoyera+ ngati ubweya wa nkhosa woyera, zoyera kwambiri kuti mbee! Ndipo maso ake anali ngati lawi la moto.+