Chivumbulutso 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Khala maso,+ ndipo limbikitsa+ otsala amene atsala pang’ono kufa, chifukwa ndapeza kuti ntchito zako sizinachitidwe mokwanira pamaso pa Mulungu wanga.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:2 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2022, ptsa. 3-4 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 55-56
2 Khala maso,+ ndipo limbikitsa+ otsala amene atsala pang’ono kufa, chifukwa ndapeza kuti ntchito zako sizinachitidwe mokwanira pamaso pa Mulungu wanga.+