Chivumbulutso 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Zimenezi zitatha, ndinaona angelo+ anayi ataimirira m’makona anayi a dziko lapansi. Iwo anali atagwira mwamphamvu mphepo zinayi+ za dziko lapansi, kuti mphepo iliyonse isawombe padziko lapansi, panyanja, kapena pamtengo uliwonse.+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:1 Nsanja ya Olonda,11/15/2013, tsa. 1312/15/2007, tsa. 161/1/1993, tsa. 612/15/1987, tsa. 7 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 113-115
7 Zimenezi zitatha, ndinaona angelo+ anayi ataimirira m’makona anayi a dziko lapansi. Iwo anali atagwira mwamphamvu mphepo zinayi+ za dziko lapansi, kuti mphepo iliyonse isawombe padziko lapansi, panyanja, kapena pamtengo uliwonse.+
7:1 Nsanja ya Olonda,11/15/2013, tsa. 1312/15/2007, tsa. 161/1/1993, tsa. 612/15/1987, tsa. 7 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 113-115