Yeremiya 25:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Taonani! Tsoka likuyenda kuchokera mu mtundu wina kupita mu mtundu wina,+ ndipo mkuntho wamphamvu udzafika kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+
32 “Yehova wa makamu wanena kuti, ‘Taonani! Tsoka likuyenda kuchokera mu mtundu wina kupita mu mtundu wina,+ ndipo mkuntho wamphamvu udzafika kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+