Chivumbulutso 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo anali kuimba+ nyimbo yokhala ngati yatsopano+ pamaso pa mpando wachifumu, pamaso pa zamoyo zinayi,+ ndi pamaso pa akulu.+ Palibe anatha kuiphunzira nyimboyo, koma 144,000+ amene anagulidwa+ padziko lapansi. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:3 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 31 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 200-201, 202-203 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, tsa. 20
3 Iwo anali kuimba+ nyimbo yokhala ngati yatsopano+ pamaso pa mpando wachifumu, pamaso pa zamoyo zinayi,+ ndi pamaso pa akulu.+ Palibe anatha kuiphunzira nyimboyo, koma 144,000+ amene anagulidwa+ padziko lapansi.
14:3 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 31 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 200-201, 202-203 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, tsa. 20