Chivumbulutso 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mngelo wina wachitatu anawatsatira, ndipo ananena mofuula kuti: “Ngati wina walambira chilombo+ ndi chifaniziro chake,+ ndipo walandira chizindikiro pamphumi kapena padzanja lake,+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:9 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 209-210 Nsanja ya Olonda,10/1/2005, ptsa. 24-251/1/1988, tsa. 16
9 Mngelo wina wachitatu anawatsatira, ndipo ananena mofuula kuti: “Ngati wina walambira chilombo+ ndi chifaniziro chake,+ ndipo walandira chizindikiro pamphumi kapena padzanja lake,+