Chivumbulutso 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 adzamwanso vinyo wosasungunula wa mkwiyo+ wa Mulungu amene akuthiridwa m’kapu ya mkwiyo wake. Ndipo adzazunzidwa+ ndi moto ndi sulufule+ pamaso pa angelo oyera, ndi pamaso pa Mwanawankhosa. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:10 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 209-211 Nsanja ya Olonda,4/15/1993, tsa. 7 Kukambitsirana, ptsa. 147-148
10 adzamwanso vinyo wosasungunula wa mkwiyo+ wa Mulungu amene akuthiridwa m’kapu ya mkwiyo wake. Ndipo adzazunzidwa+ ndi moto ndi sulufule+ pamaso pa angelo oyera, ndi pamaso pa Mwanawankhosa.
14:10 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 209-211 Nsanja ya Olonda,4/15/1993, tsa. 7 Kukambitsirana, ptsa. 147-148