Chivumbulutso 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mngelo wachinayi+ anathira mbale yake padzuwa. Ndipo dzuwa linaloledwa kutentha+ anthu ndi moto. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:8 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 225-227