Chivumbulutso 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ine Yohane, ndine amene ndinali kumva ndi kuona zinthu zimenezi. Ndipo nditamva ndi kuona, ndinagwada n’kuwerama kuti ndilambire+ pamapazi a mngelo amene anali kundionetsa zinthu zimenezi. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:8 Mapeto a Chivumbulutso, tsa. 314 Nsanja ya Olonda,8/1/1999, tsa. 14
8 Ine Yohane, ndine amene ndinali kumva ndi kuona zinthu zimenezi. Ndipo nditamva ndi kuona, ndinagwada n’kuwerama kuti ndilambire+ pamapazi a mngelo amene anali kundionetsa zinthu zimenezi.