Mawu a M'munsi
a Makolo mungachite bwino kuwerenga nkhani yakuti, “Ana Akamagwiritsa Ntchito Intaneti Zimene Makolo Ayenera Kudziwa,” mu Galamukani! ya October 2008. Mu Galamukani! ya December 2007 ndi JJanuary 2008, mungapeze nkhani zothandiza zokhudza zinthu zolaula, masewera a pa kompyuta ndiponso Intaneti.