Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 12/07 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2007
  • Nkhani Yofanana
  • Baikal Ndi Nyanja Yaikulu Kwambiri Padziko Lonse
    Galamukani!—2007
  • Kodi Ndingapewe Bwanji Kuona Zithunzi Zolaula?
    Galamukani!—2007
  • Kuchokera kwa Owerenga
    Galamukani!—2008
  • Kuchokera kwa Owerenga
    Galamukani!—2008
Onani Zambiri
Galamukani!—2007
g 12/07 tsamba 1-2

Zamkatimu

December 2007

Kodi Imfa ndi Mapeto a Zonse?

Anthu ambiri amakhulupirira kuti imfa ndi mapeto a moyo, ndiponso kuti palibe chiyembekezo chilichonse chakuti akufa adzauka. Taonani mfundo zogwira mtima zimene zili m’nkhaniyi.

3 N’chifukwa Chiyani Timaopa Imfa?

5 Kodi Imfa Ndi Mapeto a Zonse?

15 Baikal Ndi Nyanja Yaikulu Kwambiri Padziko Lonse

20 Ndalama Zinafalitsa Dzina la Mulungu

22 Mafunde Sangapose Zimenezi Ngakhale Atatalika Motani

26 Mfumu Imene Inachita Zazikulu

28 Kuchokera kwa Owerenga

29 Zochitika Padzikoli

30 Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2007

31 Kodi Mungayankhe Bwanji?

32 Pankhani ya Zimene Zimachitika Munthu Akafa—Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kusamalira Chilengedwe? 10

Kodi tiyenera kusamalira chilengedwe pa zifukwa zotani? Nanga tiyenera kuona kuti tili ndi udindo waukulu motani pankhani yosamalira chilengedwe?

Kodi Ndingapewe Bwanji Kuona Zithunzi Zolaula? 12

Pa Intaneti pali malo ambirimbiri amene amakhala ndi zithunzi zolaula zosawerengeka. Dziwani mmene mungapewere kuona zinthu zoterezi kuti zisakugwetsereni m’mavuto.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena