Mawu a M'munsi
b Kuti muzipindula kwambiri mukamawerenga Baibulo ndiponso mukamaphunzira panokha, onani mutu wakuti “Chitani Khama pa Kuwerenga” ndi wakuti “Kuphunzira Kumapindulitsa” m’buku la Pindulani ndi Sukulu ya Utumiki wa Mulungu, masamba 21 mpaka 32.