Mawu a M'munsi
a Malangizo oterewa tingawapeze m’nkhani yakuti, “Tiyenera Kugwiritsa Ntchito Intaneti Mwanzeru” mu Nsanja ya Olonda ya August 15, 2011, tsamba 3 mpaka 5. Malangizo ena ali m’nkhani yakuti, “Samalani ndi Misampha ya Mdyerekezi” komanso yakuti, “Musasunthike Popewa Misampha ya Satana” mu Nsanja ya Olonda ya August 15, 2012, tsamba 20 mpaka 29.