Mawu a M'munsi
a Ku Meriba uku ndi kosiyana ndi ku Meriba komwe kunayandikana ndi dera la Refidimu. Malowa anali ku Kadesi osati ku Masa. Koma malo onsewa anatchedwa Meriba chifukwa cha kukangana komwe kunachitikako.—Onani kabuku kakuti Onani Dziko Lokoma, patsamba 9 kapena Kabuku Kothandiza Kuphunzira Mawu a Mulungu, mutu 7.