Mawu a M'munsi
b Kuti mupeze mfundo zothandiza munthu amene akufuna kudzipha onani nkhani za mu Galamukani! zakuti: “Kodi Kudzipha Ndi Njira Yabwino Yothetsera Mavuto?” (April 2014); “Kodi Mungatani Mukakhala ndi Maganizo Ofuna Kudzipha?” (January 2012); “N’chifukwa Chiyani Anthu Amatopa Nawo Moyo?” komanso yakuti “Mutha Kupeza Thandizo” (November 8, 2001).