January Magazini Yophunzira Zimene Zili M’magaziniyi MARCH 2-8, 2026 Pitirizani Kukwaniritsa ‘Zosowa Zanu Zauzimu’ MARCH 9-15, 2026 N’zotheka Kulimbana Ndi Maganizo Ofooketsa MARCH 16-22, 2026 N’chifukwa Chiyani Timafunikira Dipo? MARCH 23-29, 2026 Kodi “Inuyo” Mungasonyeze Bwanji Kuti Mumayamikira Dipo? MARCH 30–APRIL 5, 2026 Muziphunzitsa Choonadi Mokoma Mtima MFUNDO ZOTHANDIZA POPHUNZIRA Muziyerekezera Kuti Mukuona Zomwe Zikuchitika Mukamawerenga Nkhani za M’Baibulo