September Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya September 2019 Zimene Tinganene September 2-8 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 7-8 “Wansembe Mpaka Muyaya Monga mwa Unsembe wa Melekizedeki” September 9-15 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 9-10 ‘Chithunzi cha Zinthu Zabwino Zimene Zikubwera’ September 16-22 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 11 Chikhulupiriro ndi Chofunika Kwambiri MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Mudzatani pa Nthawi ya Chilala? September 23-29 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | AHEBERI 12-13 Chilango Chimasonyeza Kuti Yehova Amatikonda September 30–October 6 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YAKOBO 1-2 Kuganizira Zoipa N’koopsa MOYO WATHU WACHIKHRISTU “Pitirizani Kuganizira Zimenezi”