November Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya November 2018 Zimene Tinganene November 5-11 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YOHANE 20-21 “Kodi Umandikonda Ine Kuposa Izi?” November 12-18 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 1-3 Mpingo Wachikhristu Unalandira Mzimu Woyera MOYO WATHU WACHIKHRISTU Tizichita Zinthu Mogwirizana Tikamalalikira M’gawo la Zinenero Zambiri November 19-25 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 4-5 Anapitiriza Kulankhula Mawu a Mulungu Molimba Mtima MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kulalikira ndi Mashelefu Kwathandiza Anthu Ambiri Padziko Lonse November 26–December 2 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 6-8 Mpingo Watsopano Wachikhristu Unayesedwa MOYO WATHU WACHIKHRISTU “Muzipereka Mphatso kwa Yehova”