December Ndandanda ya Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu ya December 2020 Zimene Tinganene December 7-13 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LEVITIKO 10-11 Tizikonda Yehova Kuposa Mmene Timakondera Achibale Athu MOYO WATHU WACHIKHRISTU Timasonyeza Chikondi Tikamachita Zinthu Mogwirizana Ndi Chilango Chochokera kwa Yehova December 14-20 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LEVITIKO 12-13 Zimene Tingaphunzire pa Malamulo Okhudza Khate December 21-27 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LEVITIKO 14-15 Timafunika Kukhala Oyera Kuti Tizilambira Mulungu Movomerezeka MOYO WATHU WACHIKHRISTU Tizigwiritsabe Ntchito Magazini December 28, 2020–January 3, 2021 CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LEVITIKO 16-17 Kodi Tsiku la Mwambo Wophimba Machimo Limakukhudzani Bwanji? MOYO WATHU WACHIKHRISTU Kodi Mungakonde Kufunsira Sukulu ya Akhristu Olalikira za Ufumu?