Zamkatimu
February 8, 2001
Kulimbikitsa Odwala
Kudwala matenda aakulu ndiponso ofoola thupi kumasokonezadi maganizo. Kodi munthu angathane nawo bwanji matenda otere?
6 Ndi Motani Mmene Mungakhalire Osangalala Ngakhale Mukudwala?
11 Kulimbana ndi Mavuto mwa Kukhala N’zolinga
17 Mavuto Oyesa Kuchita Zinthu Zambiri
20 Kupirira Mosangalala M’dziko Lotangwanitsa
Moto! Kodi Muyenera Kuuzimitsa ndi Chida Chiti? 24
Udziŵeni bwino moto ndi mmene mungauzimitsire.
Bwanji Ngati Makolo Anga Akuona Kuti Sindinafike Pokhala N’chibwenzi? 28
Kodi kukhala n’chibwenzi mudakali aang’ono kuli ndi vuto lililonse?