Za M’katimu
Mutu
1 Chifukwa Chake Yesu Anali Mphunzitsi Waluso
2 Kalata Yochokera kwa Mulungu Amene Amatikonda
6 Mphunzitsi Waluso Anatumikira Anthu Ena
8 Mulungu Ndi Wamkulu Kuposa Aliyense
10 Yesu Ali ndi Mphamvu Kuposa Ziwanda
11 Angelo a Mulungu Amatithandiza
12 Yesu Atiphunzitsa Kupemphera
13 Amene Anakhala Ophunzira a Yesu
14 Chifukwa Chake Tiyenera Kukhululukira Ena
15 Phunziro la Kukhala Wokoma Mtima
16 Kodi Chofunika Kwambiri Ndi Chiyani?
17 Mmene Tingakhalire Osangalala
18 Kodi Umakumbukira Kunena Kuti Zikomo?
19 Kodi Ndi Bwino Kuchita Ndewu?
20 Kodi Nthaŵi Zonse U mafuna Kukhala Woyamba?
21 Kodi Tiyenera Kudzitama Tikachita Zabwino?
22 Chifukwa Chake Tiyenera Kupewa Bodza
23 Chifukwa Chake Anthufe Timadwala
25 Kodi Amene Amachita Zinthu Zoipa Angasinthe?
26 Chifukwa Chake Kuchita Zinthu Zabwino Kumavuta
28 Kudziŵa Amene Uyenera Kumumvera
29 Kodi Ndi Mapwando Onse Amene Amakondweretsa Mulungu?
30 Zimene Zingatithandize Kuthetsa Mantha
34 Kodi Chimachitika Ndi Chiyani Tikamwalira?
36 Kodi Ndani Adzauka kwa Akufa? Nanga Adzakhala Kuti?
37 Kukumbukira Yehova ndi Mwana Wake
38 Chifukwa Chake Tiyenera Kukonda Yesu
39 Mulungu Anakumbukira Mwana Wake
40 Zimene Tingachite Kuti Tikondweretse Mulungu
41 Ana Amene Amakondweretsa Mulungu
42 Chifukwa Chake Tifunikira Kugwira Ntchito
43 Kodi Abale Athu ndi Alongo Athu Ndani?
44 Mabwenzi Athu Azikhala Okonda Mulungu
45 Kodi Ufumu wa Mulungu Ndi Chiyani? Zimene Tingachite Posonyeza Kuti Tikuufuna
46 Madzi Anawononga Dziko—Kodi Zidzachitikanso?