CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EZEKIELI 35-38
Gogi wa ku Magogi Awonongedwa Posachedwapa
Baibulo limafotokoza zimene zidzachitike Gogi wa ku Magogi asanawonongedwe komanso akadzawonongedwa.
Kodi chisautso chachikulu chidzayamba ndi kuwonongedwa kwa chiyani?
Kodi anthu a Yehova adzaukiridwa ndi ndani?
Kodi Yehova adzawononga Gogi wa ku Magogi pankhondo iti?
Kodi Khristu adzalamulira kwa zaka zingati?
Kodi ndingatani kuti ndidzakhale wokonzeka pamene Gogi wa ku Magogi adzaukire anthu a Mulungu?