Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 November tsamba 8
  • Zimene Tikuphunzira Kuchokera m’Buku la Yona

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zimene Tikuphunzira Kuchokera m’Buku la Yona
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • Anaphunzira pa Zolakwa Zake
    Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo
  • Muziphunzirapo Kanthu pa Zimene Munalakwitsa
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Anaphunzira pa Zolakwa Zake
    Nsanja ya Olonda—2009
  • Yona Aphunzira za Chifundo cha Yehova
    Nsanja ya Olonda—1996
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 November tsamba 8

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Zimene Tikuphunzira Kuchokera m’Buku la Yona

Yehova anachititsa kuti nkhani zosiyanasiyana za amuna ndi akazi okhulupirika zilembedwe m’Mawu ake n’cholinga choti tiphunzirepo kanthu. (Aroma 15:4) Kodi mwaphunzira zotani m’buku la Yona? Onerani vidiyo yakuti Kulambira kwa Pabanja: Yona Anaphunzira Kuti Mulungu Ndi Wachifundo, kenako yankhani mafunso otsatirawa:

  • Kodi ofalitsa atatu a m’vidiyoyi anakumana ndi mavuto otani?

  • Kodi mfundo za m’buku la Yona zingatithandize bwanji tikapatsidwa uphungu kapena tikauzidwa kuti tisiye kuchita utumiki winawake? (1 Sam. 16:7; Yona 3:1, 2)

  • Kodi nkhani ya Yona ingatithandize bwanji kuti tiziwaona moyenerera anthu a m’gawo lathu? (Yona 4:11; Mat. 5:7)

  • Kodi zimene zinachitikira Yona zingatithandize bwanji ngati tikudwala matenda aakulu? (Yona 2:1, 2, 7, 9)

  • Kodi mwaphunzira zotani m’vidiyoyi zomwe zikusonyeza kuti kuwerenga Baibulo komanso kuganizira zimene tawerengazo n’kofunika kwambiri?

M’bale akuoneka wosasangalala chifukwa anachotsedwa pa udindo; mlongo akuganiza kuti salandiridwa bwino mu utumiki; mlongo akufotokozeredwa za vuto lake ndi dokotala
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena