Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb17 November tsamba 4
  • Muziphunzirapo Kanthu pa Zimene Munalakwitsa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Muziphunzirapo Kanthu pa Zimene Munalakwitsa
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Nkhani Yofanana
  • Zimene Tikuphunzira Kuchokera m’Buku la Yona
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Anaphunzira pa Zolakwa Zake
    Tsanzirani Chikhulupiriro Chawo
  • Anaphunzira pa Zolakwa Zake
    Nsanja ya Olonda—2009
  • Yona Aphunzira za Chifundo cha Yehova
    Nsanja ya Olonda—1996
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
mwb17 November tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | OBADIYA 1–YONA 4

Muziphunzirapo Kanthu pa Zimene Munalakwitsa

Nkhani ya Yona imasonyeza kuti Yehova satisiya tikalakwitsa zinazake. M’malomwake, amafuna kuti tiphunzirepo kanthu pa zimene talakwitsazo n’kusintha.

Yona 1:3

Kodi Yona anatani Yehova atamupatsa ntchito yoti agwire?

Njira yapanyanja kuchokera ku Yopa kupita ku Tarisi

Yona 2:1-10

Kodi Yona anapempha chiyani ndipo Yehova anayankha bwanji pemphero lakelo?

Yona akupemphera mphepete mwanyanja

Yona 3:1-3

Kodi Yona anasonyeza bwanji kuti anaphunzirapo kanthu pa zimene analakwitsa?

Njira yochokera ku Yopa kupita ku Tarisi
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena