Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb16 December tsamba 4
  • Mesiya Anakwaniritsa Ulosi

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mesiya Anakwaniritsa Ulosi
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
  • Nkhani Yofanana
  • A7-C Zinthu Zikuluzikulu Zimene Yesu Anachita Ali Padziko Lapansi—Utumiki Waukulu wa Yesu MʼGalileya (Gawo 1)
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • A7-B Zinthu Zikuluzikulu Zimene Yesu Anachita Ali Padziko Lapansi—Chiyambi cha Utumiki wa Yesu
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • A7-D Zinthu Zikuluzikulu Zimene Yesu Anachita Ali Padziko Lapansi—Utumiki Waukulu wa Yesu MʼGalileya (Gawo 2)
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
  • Chozizwitsa Chachiwiri Chimene Yesu Anachita ku Kana
    Yesu—Ndi Njira, Choonadi ndi Moyo
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2016
mwb16 December tsamba 4

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YESAYA 6-10

Mesiya Anakwaniritsa Ulosi

Losindikizidwa

Kudakali zaka zambiri kuti Yesu abadwe, Yesaya ananeneratu kuti Mesiya adzalalikira “m’chigawo cha Yorodano, ku Galileya kumene kunali kukhala anthu a mitundu ina.” Yesu anakwaniritsa ulosi umenewu chifukwa analalikira uthenga wabwino m’chigawo chonse cha Galileya.—Yes. 9:1, 2.

Mapu a Galileya
  • Mbiya ya vinyo

    Anachita chozizwitsa chake choyamba pa ukwati winawake—Yoh. 2:1-11 (ku Kana)

  • Atumwi 12

    Anasankha atumwi ake—Maliko 3:13, 14 (kufupi ndi ku Kaperenao)

  • Yesu akuphunzitsa anthu

    Analalikira ulaliki wake wa paphiri—Mat. 5:1–7:27 (pafupi ndi ku Kaperenao)

  • Mnyamata waukitsidwa

    Anaukitsa mwana yekhayo wa mkazi wina wamasiye—Luka 7:11-17 (ku Naini)

  • Yesu waonekera kwa ophunzira ake ataukitsidwa

    Anaonekera kwa ophunzira ake oposa 500 pambuyo poti waukitsidwa—1 Akor. 15:6 (ku Galileya)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena