Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 July tsamba 3
  • Kodi Chofunika N’chiyani Kuti Munthu Akhale Wotsatira wa Yesu?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Chofunika N’chiyani Kuti Munthu Akhale Wotsatira wa Yesu?
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Musamayang’ane “Zinthu za M’mbuyo”
    Nsanja ya Olonda—2012
  • Kuganizira Zoipa N’koopsa
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Zisangalalo ndi Zipatso za Utumiki Waufumu
    Imbirani Yehova Zitamando
  • Utumiki Wothandiza Anthu pa Nthawi ya Mavuto
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 July tsamba 3

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | LUKA 8-9

Kodi Chofunika N’chiyani Kuti Munthu Akhale Wotsatira wa Yesu?

9:62

Kuti munthu amene ankalima ndi pulawo alime mizere yowongoka, sankafunika kuyang’ana zinthu zakumbuyo. Mofanana ndi zimenezi, Mkhristu sayenera kusokonezedwa ndi zinthu za m’dzikoli zimene anazisiya.​—Afil. 3:13.

Tikakumana ndi mavuto n’zosavuta kuyamba kuganiza za nthawi imene tinali tisanaphunzire choonadi n’kumanena kuti, ‘Koma kale likanati lizibwerera!’ Munthu akamachita zimenezi amakhala akungoganizira za zinthu zabwino zimene ankapeza koma saganizira za mavuto amene ankakumana nawo. Izi ndi zomwe Aisiraeli anachita atachoka ku Iguputo. (Num. 11:5, 6) Tikamaganizira kwambiri zinthu za m’mbuyo, tikhoza kukopeka n’kuyamba kuchita zimene tinasiya. Choncho ndi nzeru kumaganizira madalitso amene tikupeza panopo, komanso amene tidzapeze m’tsogolo mu Ufumu wa Mulungu.​—2 Akor. 4:16-18.

Munthu amene akulima ndi pulawo akungoyang’ana kutsogolo kuti asasokonezedwe ndi zinthu zakumbuyo
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena