Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 September tsamba 6
  • Kuganizira Zoipa N’koopsa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kuganizira Zoipa N’koopsa
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Mayesero
    Galamukani!—2017
  • “Khalani Oyera”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Yehova Analenga Zamoyo Padziko Lapansi
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Musalole Kuti Zilakolako Zoipa Zizikulamulirani
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 September tsamba 6
M’bale akuganizira mayesero osiyanasiyana monga ndalama, galimoto yodula, fodya komanso mkazi yemwe akumukopa

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | YAKOBO 1-2

Kuganizira Zoipa N’koopsa

1:14, 15

Maganizo oipa akakubwererani, muzichita zinthu zotsatirazi:

  • Muziwachotsa msanga n’kuyamba kuganizira zinthu zina.​—Afil. 4:8

  • Muziganizira mavuto amene angabwere ngati mutachita zoipazo.​—Deut. 32:29

  • Muzipemphera.​—Mat. 26:41

Maganizo oipa akandibwerera, kodi ndi zinthu zolimbikitsa ziti zomwe ndingayambe kuganizira?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena