Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yosamalira Makolo Achikulire?
    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
      • Yesu atangotsala pang’ono kuphedwa, anasankhiratu munthu woti azidzasamalira mayi ake Mariya, yemwe ayenera kuti anali wamasiye.—Yohane 19:26, 27.a

  • Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yosamalira Makolo Achikulire?
    Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
    • a Pa nkhaniyi, buku lina lofotokoza za Baibulo limanena kuti: “Zikuoneka kuti panali patapita nthawi kuchokera pamene Yosefe [mwamuna wake wa Mariya] anamwalira ndipo Yesu ndi amene ankasamalira Mariya. Koma popeza kuti Yesu anali atatsala pang’ono kuphedwa, n’kutheka kuti ankada nkhawa za amene adzasamalire mayi akewo. . . Apa Khristu anapereka chitsanzo chabwino kwa ana kuti azisamalira makolo awo achikulire.”—The NIV Matthew Henry Commentary in One Volume, pages 428-429.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena