MARCH 11-17
SALIMO 18
Nyimbo Na. 148 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
1. “Yehova Ndi . . . Amene Amandipulumutsa”
(10 min.)
Yehova ali ngati thanthwe, malo achitetezo komanso chishango (Sl 18:1, 2; w09 5/1 14 ¶4-5)
Yehova amamva kulira kwathu kopempha thandizo (Sl 18:6; it-2 1161 ¶7)
Yehova amachitapo kanthu kuti atithandize (Sl 18:16, 17; w22.04 3 ¶1)
Yehova akhoza kusankha kutichotsera mayesero ngati mmene nthawi zina ankachitira ndi Davide. Komabe, nthawi zambiri Mulungu amapereka “njira yopulumukira” mwa kutipatsa zimene timafunikira kuti tithe kupirira mayeserowo.—1Ak 10:13.
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Sl 18:10—N’chifukwa chiyani yemwe analemba salimoli ananena kuti Yehova anakwera pakerubi? (it-1 432 ¶2)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Sl 18:20-39 (th phunziro 10)
4. Kukoma Mtima—Zomwe Yesu Anachita
(7 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO, kenako kambiranani kabuku ka lmd phunziro 3 mfundo 1-2.
5. Kukoma Mtima—Zomwe Mungachite Potsanzira Yesu
(8 min.) Nkhani yokambirana kuchokera mu kabuku ka lmd phunziro 3 mfundo 3-5 ndi “Onaninso Malemba Awa.”
Nyimbo Na. 60
6. Zofunika Pampingo
(5 min.)
7. Vidiyo ya Zimene Gulu Lathu Lachita ya March
(10 min.) Onerani VIDIYOYI.
8. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) bt mutu 7 ¶1-8, bokosi patsamba 53