Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb24 March tsamba 5
  • March 18-24

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • March 18-24
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Kabuku ka Msonkhano—2024
mwb24 March tsamba 5

MARCH 18-24

MASALIMO 19-21

Nyimbo Na. 6 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

M’bale akuyang’ana kumwamba komwe kwawala ndi nyenyezi.

1. “Zinthu Zakumwamba Zikulengeza Ulemerero wa Mulungu”

(10 min.)

Chilengedwe chimalengeza ulemerero wa Yehova (Sl 19:1; w04 1/1 8 ¶1-2)

Dzuwa ndi lochititsa chidwi kwambiri (Sl 19:4-6; w04 6/1 11 ¶8-10)

Tiziphunzirapo kanthu pa zinthu zimene Mulungu analenga (Mt 6:28; g95 11/8 23 ¶2)


ZIMENE MUNGACHITE PA KULAMBIRA KWA PABANJA: Onani zinthu zinazake zachilengedwe, kenako kambiranani zimene mukuphunzirapo zokhudza Yehova.

2. Mfundo Zothandiza

(10 min.)

  • Sl 19:7-9​—N’chifukwa chiyani tinganene kuti mavesiwa ndi chitsanzo chabwino cha mmene ndakatulo zina za Chiheberi zinkalembedwera? (it-1 1073)

  • Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?

3. Kuwerenga Baibulo

(4 min.) Sl 19:1-14 (th phunziro 11)

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

4. Ulendo Woyamba

(3 min.) KULALIKIRA M’MALO OPEZEKA ANTHU AMBIRI. Mugawireni kapepala koitanira anthu ku Chikumbutso, ndipo gwiritsani ntchito webusaiti ya jw.org kuti mupeze malo amene mwambowu ukachitikire kufupi ndi kwawo. (lmd phunziro 2 mfundo 3)

5. Ulendo Woyamba

(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Landirani munthu amene wabwera ku Chikumbutso chifukwa choti anapeza kapepala koitanira anthu ku mwambowu pakhomo la nyumba yake. Kambiranani zoti mudzakumanenso kuti mudzayankhe mafunso ake. (lmd phunziro 3 mfundo 4)

6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupirira

(5 min.) Nkhani. ijwfq 45​—Mutu: N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Amachita Mwambo wa Mgonero wa Ambuye Mosiyana ndi Zipembedzo Zina? (th phunziro 6)

MOYO WATHU WA CHIKHRISTU

Nyimbo Na. 141

7. Muzilimbitsa Chikhulupiriro Chanu Pogwiritsa Ntchito Zinthu za M’chilengedwe

(15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani VIDIYO. Kenako funsani omvera funso ili:

Kodi zolengedwa zosiyanasiyana zimakuthandizani bwanji kukhulupirira kwambiri Mlengi?

8. Phunziro la Baibulo la Mpingo

(30 min.) bt mutu 7 ¶9-13, bokosi patsamba 56

Mawu Omaliza (3 min.) | Nyimbo Na. 127 ndi Pemphero

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena