MARCH 25-31
SALIMO 22
Nyimbo Na. 19 ndi Pemphero | Mawu Oyamba (1 min.)
Asilikali akuchita maere pa malaya akunja a Yesu.
1. Baibulo Linaneneratu Zinthu Zina Zokhudza Imfa ya Yesu
(10 min.)
Anthu adzaona ngati Yesu wasiyidwa ndi Mulungu (Sl 22:1; w11 8/15 15 ¶16)
Yesu adzanyozedwa (Sl 22:7, 8; w11 8/15 15 ¶13)
Adzachita maere pa zovala za Yesu (Sl 22:18; w11 8/15 15 ¶14; onani chithunzi chapachikuto)
2. Mfundo Zothandiza
(10 min.)
Sl 22:22—Kodi masiku ano tingatsanzire wolemba masalimo m’njira ziwiri ziti? (w06 11/1 29 ¶7; w03 9/1 20 ¶1)
Kodi ndi mfundo ziti zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
3. Kuwerenga Baibulo
(4 min.) Sl 22:1-19 (th phunziro 2)
4. Ulendo Woyamba
(3 min.) KUNYUMBA NDI NYUMBA. (lmd phunziro 4 mfundo 4)
5. Ulendo Wobwereza
(4 min.) KULALIKIRA MWAMWAYI. Chitani ulendo wobwereza kwa mnzanu amene analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso. (lmd phunziro 4 mfundo 3)
6. Nkhani
(5 min.) w20.07 12-13 ¶14-17—Mutu: Kodi Maulosi a M’Baibulo Amatithandiza Bwanji Kukhala ndi Chikhulupiriro Cholimba? (th phunziro 20)
Nyimbo Na. 95
7. Zofunika Pampingo
(15 min.)
8. Phunziro la Baibulo la Mpingo
(30 min.) bt mutu 7 ¶14-18, bokosi patsamba 57-58