Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • sn nyimbo 25
  • Chizindikiro cha Ophunzira a Khristu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Chizindikiro cha Ophunzira a Khristu
  • Imbirani Yehova
  • Nkhani Yofanana
  • “Mulungu Ndiye Chikondi”
    Imbirani Yehova
  • “Mulungu Ndi Chikondi”
    Imbirani Yehova Mosangalala
  • Chitsimikiziro cha Kukhala Ophunzira
    Imbirani Yehova Zitamando
  • “Tizisonyezana Chikondi Chenicheni M’zochita Zathu”
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2017
Onani Zambiri
Imbirani Yehova
sn nyimbo 25

Nyimbo 25

Chizindikiro cha Ophunzira a Khristu

Losindikizidwa

(Yohane 13:34, 35)

1. Pali lamulo tilimvere

Kuti tikhale Akhristu

Lamuloli ndi lakumwamba

Polimvera, tikondana.

Chikondi cha Khristu Ambuye

Chinam’chititsa ’tifere.

Tikatsatira chitsanzo chake

Tisonyeza tili ake.

2. Chikondi choona n’chosatha

Chimathandiza ofo’ka.

Ndipo chilingati ngongole,

Yobweza potumikira.

Palibe kwina tingapeze

Otikonda moteremu.

Chikondichi ndi chodalirika,

Motero tizikondana.

(Onaninso Aroma 13:8; 1 Akor. 13:8; Yak. 2:8; 1 Yoh. 4:10, 11.)

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena